Genesis 45:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe sanakhoza kudziletsa pamaso pa onse amene anaima naye: nati, Turutsa anthu onse pamaso panga. Ndipo panalibe munthu pamodzi ndi iye pamene Yosefe anadziululira yekha kwa abale ace.

Genesis 45

Genesis 45:1-10