Genesis 41:55 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene dziko lonse la Aigupto linali ndi njala, anthu anapfuulira Farao awapatse cakudya; ndipo Farao anati kwa Aaigupto onse, Pitani kwa Yosefe: cimene iye anena kwa inu citani.

Genesis 41

Genesis 41:45-57