Genesis 41:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zinayamba kufika zaka zisanu ndi ziwiri za njala, monga ananena Yosefe; ndipo munali njala m'maiko monse; koma m'dziko lonse la Aigupto munali cakudya.

Genesis 41

Genesis 41:52-57