Genesis 31:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti wafunafuna monse ndiri nazo, kodi wapeza ciani pa zinthu za m'nyumba mwako? Tafika naco apa pa abale anga ndi ako, kuti aweruze pa ife tonse awiri.

Genesis 31

Genesis 31:35-40