Genesis 31:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakwiya Yakobo namkalipira Labani: ndipo Yakobo anayankha nati kwa Labani, Kodi ndacimwa ciani? ucimo wanga nguti, kuti unanditsatatsata ine pambuyo panga?

Genesis 31

Genesis 31:27-38