Genesis 29:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenganso pakati nabala mwana wamwamuna; nati, Tsopano ndidzamyamikira Yehova; cifukwa cace anamucha dzina lace Yuda; pamenepo analeka kubala.

Genesis 29

Genesis 29:32-35