Genesis 29:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenganso pakati nabala mwana wamwamuna, nati, Tsopano lino mwamuna wanga adzadziphatika kwa ine cifukwa ndambalira iye ana amuna atatu; cifukwa cace anamucha dzina lace Levi.

Genesis 29

Genesis 29:25-35