Genesis 28:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake anamlola Yakobo amuke, ndipo ananka ku Padanaramu kwa Labani, mwana wace wa Betuele Msuriya, mlongo wace wa Rebeka, amai wao wa Yakobo ndi Esau.

Genesis 28

Genesis 28:1-11