Genesis 28:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akupatse iwe mdalitso wa Abrahamu, iwe ndi mbeu zako pamodzi nawe: kuti ulowe m'dziko limene ukhalamo mlendo, limene Mulungu anampatsa Abrahamu.

Genesis 28

Genesis 28:1-14