Genesis 27:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rebeka ananena kwa Yakobo mwana wace, nati, Taona ndinamva atate wako alinkunena ndi Esau mkuru wako kuti,

Genesis 27

Genesis 27:1-14