Genesis 27:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamva Rebeka pamene Isake ananena ndi Esau mwana wace. Ndipo Esau ananka kuthengo kukasaka nyama ndi kubwera nayo.

Genesis 27

Genesis 27:1-8