Genesis 27:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Esau anamva mau a atate wace Isake, analira ndi kulira kwakukuru ndi kowawa kopambana, nati kwa atate wace, Mundidalitse ine, inenso atate wanga.

Genesis 27

Genesis 27:30-37