Genesis 27:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake ananthunthumira ndi kunthunthumira kwakukuru, nati, Ndani uja anatenga nyama, nadza nayo kwa ine, ndipo ndadyako zonse usadaloweiwe, ndipondamdalitsaiye? inde, adzadalitsika.

Genesis 27

Genesis 27:23-40