Genesis 27:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake anati kwa mwana wace, Unaipeza msanga bwanji mwana wanga? Ndipo anati, Cifukwa kuti Yehova Mulungu wanu anandiyendetsa ine bwino.

Genesis 27

Genesis 27:11-27