Genesis 27:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anati kwa atate wace, Ndine Esau mwana wanu wamkuru; ndacita monga mwandiuza ine; ukanitu, khalani tsonga, idyani nyama yanga kuti moyo wanu undidalitse ine.

Genesis 27

Genesis 27:9-24