Genesis 22:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu anati, Mwana wanga, Mulungu adzadzifunira yekha mwana wa nkhosa wa nsembe yopsereza; nayenda pamodzi onse awiri.

Genesis 22

Genesis 22:1-15