Genesis 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu analowa msanga m'hema wace kwa Sara, nati, Konza msanga miyeso itatu ya ufa wosalala, nuumbe, nupange mikate.

Genesis 18

Genesis 18:1-15