Genesis 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzatenga cakudya pang'ono, nimutonthoze mitima yanu; mutatero mudzapitirira, cifukwa mwafika kwa kapolo wanu. Ndipo anati, Cita comweco monga momwe wanena.

Genesis 18

Genesis 18:1-13