Genesis 18:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Mbuyanga, ngatitu ndikapeza ufulu pamaso panu, musapitiriretu pa kapolo wanu;

4. nditengetu madzi pang'ono, ndikusambitseni mapazi anu, mupumule pansi pa mtengo;

5. ndipo ndidzatenga cakudya pang'ono, nimutonthoze mitima yanu; mutatero mudzapitirira, cifukwa mwafika kwa kapolo wanu. Ndipo anati, Cita comweco monga momwe wanena.

Genesis 18