Genesis 16:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Hagara, mdzakazi wace wa Sarai, ufumira kuti? Unka kuti? Ndipo anati, Ndithawa ine kumaso kwace kwa wakuka wanga Sarai.

Genesis 16

Genesis 16:7-13