Genesis 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abramu anasuntha hema wace nafika nakhala pa mitengo yathundu ya pa Mamre, imene iri m'Hebroni, nammangira Yehova kumeneko guwa la nsembe.

Genesis 13

Genesis 13:15-18