Genesis 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Tiyeni, timange mudzi ndi nsanja, pamutu pace pafikire kumwamba; ndipo tidzipangire ife tokha dzina kuti tisabalalike pa dziko lonse lapansi.

Genesis 11

Genesis 11:1-10