Genesis 11:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananenana wina ndi wina, Tiyeni tipange njerwa, tiziocetse. Ndipo anali ndi njerwa naziyesa miyala, ndi katondo anayesa matope.

Genesis 11

Genesis 11:1-13