Genesis 11:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo dziko lapansi linali la cinenedwe cimodzi ndi cilankhulidwe cimodzi.

2. Ndipo panali pamene anayendayenda ulendo kum'mawa, anapeza cigwa m'dziko la Sinara, ndipo anakhala kumeneko.

Genesis 11