Genesis 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Abramu, Turuka iwe m'dziko lako, ndi kwa abale ako, ndi ku nyumba ya atate wako, kunka ku dziko limene ndidzakusonyeza iwe;

Genesis 12

Genesis 12:1-11