Genesis 10:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. ndi Ahivi, ndi Aariki, ndi Asini;

18. ndi Aaravadi, ndi Aazemari, ndi Ahamati; pambuyo pace pamenepo ndipo mabanja a Akanani anafalikira.

19. Ndipo malire a Akanani anayamba pa Sidoni, pakunka ku Gerari ndi ku Gaza; pakunka ku Sodomu, ndi ku Gomora, ndi Adima, ndi Zeboimu, kufikira ku Lasa.

Genesis 10