Genesis 10:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire a Akanani anayamba pa Sidoni, pakunka ku Gerari ndi ku Gaza; pakunka ku Sodomu, ndi ku Gomora, ndi Adima, ndi Zeboimu, kufikira ku Lasa.

Genesis 10

Genesis 10:10-23