Ezekieli 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo diso langa silidzalekerera, wosacita cifundo Ine, ndidzakubwezera monga mwa njira zako, ndi zonyansa zako zidzakhala pakati pako; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova wakukantha.

Ezekieli 7

Ezekieli 7:5-10