Ezekieli 7:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Sula unyolo, popeza dziko ladzala ndi mirandu yamwazi, ndi mudzi wadzala ndi ciwawa.

24. Cifukwa cace ndidzabwera nao amitundu oipitsitsa, ndipo iwo adzalandira nyumba zao ngati colowa, ndidzaleketsanso kudzikuza kwa amphamvu, kuti adetsedwe malo ao opatulika.

25. Cionongeko cirinkudza, adzafunafuna mtendere, koma palibe.

Ezekieli 7