Ezekieli 7:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndidzabwera nao amitundu oipitsitsa, ndipo iwo adzalandira nyumba zao ngati colowa, ndidzaleketsanso kudzikuza kwa amphamvu, kuti adetsedwe malo ao opatulika.

Ezekieli 7

Ezekieli 7:23-25