Ezekieli 43:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nutengeko mwazi wace, ndi kupaka pa nyanga zinai za guwa, ndi pa ngondya zinai za phaka, ndi pa mkuzi wace pozungulira; motero uliyeretse ndi kulicitira cotetezera.

Ezekieli 43

Ezekieli 43:13-23