Ezekieli 43:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Upatse ansembe Alevi, a mbeu ya Zadoki, okhala pafupi ndi Ine, kunditumikira Ine, ati Ambuye Yehova, mwana wa ng'ombe, akhale wa nsembe yaucimo.

Ezekieli 43

Ezekieli 43:14-27