Ezekieli 41:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ziundo, ndi mazenera a made okhazikika, ndi makonde am'mwamba akuzinga zipinda zosanjikizana zao zitatu, pandunji pa ciundo, ocinga ndi matabwa pozungulira pace, kuyambira pansi kufikira kumazenera; koma mazenera anaphimbika;

Ezekieli 41

Ezekieli 41:15-21