Ezekieli 41:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anayesa m'litali mwace nyumbayo inali kutsogolo kwace kwa mpata wokhala cakuno cace, ndi makonde ace am'mwamba, cakuno ndi cauko, mikono zana limodzi, ndi Kacisi wa m'katimo, ndi makonde a kubwalo;

Ezekieli 41

Ezekieli 41:14-22