Ezekieli 40:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuka nane komweko, ndipo taona, panali munthu, maonekedwe ace ngati amkuwa, ndi cingwe cabwazi m'dzanja lace, ndi bango loyesa nalo, naima kucipata iye.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:1-13