Ezekieli 40:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka ca makumi awiri ndi zisanu ca undende wathu, poyamba caka, tsiku lakhumi lamwezi, caka cakhumi ndi zinai atakantha mudziwo, tsiku lomwelo, dzanja la Mulungu linandikhalira; ndipo anamuka nane komweko.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:1-6