Ezekieli 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo utatsiriza awa, ugonerenso mbali yako ya kumanja, ndi kusenza mphulupulu ya nyumba ya Yuda; ndakuikira masiku makumi anai, kuliyesa tsiku limodzi ngati caka cimodzi.

Ezekieli 4

Ezekieli 4:1-16