Ezekieli 4:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ine ndakuikira zaka za mphulupulu yao ngati masiku, ndiwo masiku mazana atatu mphambu makumi asanu ndi anai, kuti usenze mphulupulu ya nyumba ya Israyeli.

Ezekieli 4

Ezekieli 4:1-15