Ezekieli 39:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzasenza manyazi ao, ndi zolakwa zao zonse, zimene anandilakwira nazo, pokhala mosatekeseka iwo m'dziko lao, opanda wina wakuwaopsa;

Ezekieli 39

Ezekieli 39:24-27