Ezekieli 39:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Tsopano ndidzabweza undende wa Yakobo, ndi kucitira cifundo nyumba yonse ya Israyeli, ndipo ndidzacitira dzina langa loyera nsanje.

Ezekieli 39

Ezekieli 39:22-29