Ezekieli 38:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Ambuye Yehova, Kodi iwe ndiwe iye amene ndinanena za iye masiku akale mwa atumiki anga aneneri a Israyeli, akunenera masiku aja za zaka za m'tsogolo, kuti ndidzabwera nawe kulimbana nao?

Ezekieli 38

Ezekieli 38:14-23