Ezekieli 35:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo udzadziwa kuti Ine Yehova ndidamva zamwano zako zonse udazinena pa mapiri a Israyeli, ndi kuti, Apasuka, apatsidwa kwa ife tiwadye.

Ezekieli 35

Ezekieli 35:10-15