Ezekieli 30:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wabadwa ndi munthu iwe, ndatyola dzanja la Parao mfumu ya Aigupto, ndipo taona, silinamangidwa kuti lipole, kulikulunga ndi nsaru, kulilimbitsa ligwire lupanga.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:18-26