Ezekieli 30:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaphwetsa mitsinje, ndi kugulira dziko m'dzanja la anthu oipa, ndipo ndidzalisandutsa likhale dziko lopasuka, ndi zonse ziri m'mwemo mwa dzanja la alendo; Ine Yehova ndacinena.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:9-14