Ezekieli 30:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye ndi anthu ace pamodzi naye, woopsa amitundu, adzatengedwa aliononge dzikolo, nadzasololera Aigupto malupanga ao, ndi kudzaza dziko ndi ophedwa.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:3-13