Ezekieli 27:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, Takwezera Turo nyimbo ya maliro;

3. nuti kwa Turo, Iwe wakukhala polowera m'nyanja, wakucita malonda ndi mitundu ya anthu m'zisumbu zambiri, atero Ambuye Yehova, Iwe, Turo, wati, Ine ndine wokongola wangwiro.

4. M'mphepete mwako muli m'kati mwa nyanja, iwo anakumanga iwe anakonza kukongola kwako kukhale kwangwiro.

Ezekieli 27