Ezekieli 27:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yuda ndi dziko la Israyeli anagulana nawe malonda, anagula malonda ako ndi tirigu wa ku Miniti, ndi zozuna, ndi uci, ndi mafuta, ndi mafuta amankhwala.

Ezekieli 27

Ezekieli 27:16-18