Ezekieli 22:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Analandira mphotho mwa iwe kukhetsa mwazi, walandira phindu loonjezerapo, wanyengerera anansi ako ndi kuwazunza, ndipo wandiiwala Ine, ati Ambuye Yehova.

Ezekieli 22

Ezekieli 22:5-13