Ezekieli 19:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma unazulidwa mwaukali, unaponyedwa pansi ndi mphepo ya kum'mawa, inaumitsa zipatso zace, ndodo zace zolimba zinatyoka ndi kuuma, moto unazitha.

Ezekieli 19

Ezekieli 19:7-14