Ezekieli 18:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Moyo wocimwawo ndiwo udzafa; mwana sadzasenza mphulupulu zaatate wace, ndi atate sadzasenza mphulupulu za mwana; cilungamo ca wolungama cidzamkhalira, ndi coipa ca woipa cidzamkhalira,

Ezekieli 18

Ezekieli 18:15-25